Deuteronomo 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mungaiwale amene anakuyendetsani m’chipululu chachikulu ndi chochititsa mantha,+ chokhala ndi njoka zapoizoni,+ zinkhanira ndiponso dziko louma lopanda madzi. Amenenso anakutulutsirani madzi pamwala wolimba ngati nsangalabwi.+ Salimo 107:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Amasandutsa mitsinje kukhala chipululu,+Ndiponso akasupe a madzi kukhala malo opanda madzi.+
15 Mungaiwale amene anakuyendetsani m’chipululu chachikulu ndi chochititsa mantha,+ chokhala ndi njoka zapoizoni,+ zinkhanira ndiponso dziko louma lopanda madzi. Amenenso anakutulutsirani madzi pamwala wolimba ngati nsangalabwi.+