Miyambo 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aliyense wopusa sayenera moyo wawofuwofu.+ Ndiye kuli bwanji kuti wantchito alamulire akalonga!+ Mlaliki 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndaonapo antchito atakwera pamahatchi,* koma akalonga akuyenda pansi ngati antchito.+ Yesaya 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzaika anyamata kuti akhale akalonga awo ndipo anthu ankhanza adzawalamulira.+