Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 3:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pamenepo Yowabu anapita kwa mfumu n’kunena kuti: “N’chiyani chimene mwachitachi?+ Abineri anabwera kwa inu. N’chifukwa chiyani mwamulola kuti anyamuke ndi kupita mwamtendere?

  • 2 Samueli 3:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Ine lero ndafooka ngakhale kuti ndine mfumu yodzozedwa,+ ndipo ine ndikuona kuti amuna awa, ana a Zeruya,+ achita nkhanza kwambiri.+ Yehova abwezere aliyense wochita zinthu zoipa mogwirizana ndi kuipa kwake.”+

  • Mlaliki 10:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndaonapo antchito atakwera pamahatchi,* koma akalonga akuyenda pansi ngati antchito.+

  • Yesaya 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Anthu azidzalamulirana mwankhanza, ndipo munthu azidzachitira nkhanza munthu mnzake.+ Mnyamata adzaukira nkhalamba,+ ndipo wonyozeka adzaukira wolemekezeka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena