Salimo 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndidzagona pansi ndi kupeza tulo.Ndidzadzuka ndithu, pakuti Yehova amandithandiza.+ Salimo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzagona pansi ndi kupeza tulo mu mtendere,+Pakuti inu nokha Yehova mumandichititsa kukhala wotetezeka.+ Miyambo 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Lidzakutsogolera ukamayenda,+ lidzakulondera ukamagona,+ ndipo ukadzuka, lidzakusamalira.
8 Ndidzagona pansi ndi kupeza tulo mu mtendere,+Pakuti inu nokha Yehova mumandichititsa kukhala wotetezeka.+