2 Mbiri 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 pakuti zombo za mfumu zinkapita ku Tarisi+ limodzi ndi atumiki a Hiramu.+ Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombo za ku Tarisizo zinkabweretsa golide, siliva,+ minyanga ya njovu,+ anyani, ndi mbalame zotchedwa pikoko.+ Salimo 107:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Anthu amene amayenda m’zombo panyanja,+Amene amachita malonda pamadzi ambiri,+
21 pakuti zombo za mfumu zinkapita ku Tarisi+ limodzi ndi atumiki a Hiramu.+ Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombo za ku Tarisizo zinkabweretsa golide, siliva,+ minyanga ya njovu,+ anyani, ndi mbalame zotchedwa pikoko.+