Yoswa 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye anayankha kuti: “Ndidalitseni, poti mwandipatsa malo a kum’mwera, tsopano mundipatsenso Guloti-maimu.”* Pamenepo Kalebe anam’patsa Guloti Wakumtunda ndi Guloti Wakumunsi.+
19 Iye anayankha kuti: “Ndidalitseni, poti mwandipatsa malo a kum’mwera, tsopano mundipatsenso Guloti-maimu.”* Pamenepo Kalebe anam’patsa Guloti Wakumtunda ndi Guloti Wakumunsi.+