Ekisodo 35:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Akazi onse aluso+ anawomba nsalu ndi manja awo, ndipo anali kubweretsabe zingwe zopota za ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi nsalu zabwino kwambiri.
25 Akazi onse aluso+ anawomba nsalu ndi manja awo, ndipo anali kubweretsabe zingwe zopota za ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira, ulusi wofiira kwambiri ndi nsalu zabwino kwambiri.