Salimo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndi amene akuyenda mosalakwitsa zinthu,+ amene amachita chilungamo,+Ndi kulankhula zoona mumtima mwake.+ Salimo 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Aliyense wopanda mlandu m’manja mwake ndi woyera mumtima mwake,+Amene sanaone Moyo wanga ngati wopanda pake,+Kapena kulumbira mwachinyengo.+ Salimo 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ubwenzi wolimba ndi Yehova ndi wa anthu amene amamuopa,+Pangano lakenso ndi la anthu oterowo, ndipo iye amawadziwitsa panganolo.+
2 Ndi amene akuyenda mosalakwitsa zinthu,+ amene amachita chilungamo,+Ndi kulankhula zoona mumtima mwake.+
4 Aliyense wopanda mlandu m’manja mwake ndi woyera mumtima mwake,+Amene sanaone Moyo wanga ngati wopanda pake,+Kapena kulumbira mwachinyengo.+
14 Ubwenzi wolimba ndi Yehova ndi wa anthu amene amamuopa,+Pangano lakenso ndi la anthu oterowo, ndipo iye amawadziwitsa panganolo.+