Deuteronomo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ monga mmene Yehova Mulungu wako anakulamulira, kuti masiku ako atalike, ndi kuti zinthu zikuyendere bwino+ m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa. Miyambo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ukatero, udzakhala ndi masiku ochuluka, moyo wazaka zambiri,+ ndi mtendere.+
16 “‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako+ monga mmene Yehova Mulungu wako anakulamulira, kuti masiku ako atalike, ndi kuti zinthu zikuyendere bwino+ m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa.