Miyambo 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mawu onse otuluka pakamwa panga ndi olungama.+ Pa mawu anga palibe zokhota kapena zopotoka.+ 1 Petulo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chotero, lekani zoipa zonse,+ zachinyengo zonse, zachiphamaso, kaduka ndi mtundu uliwonse wa miseche.+
2 Chotero, lekani zoipa zonse,+ zachinyengo zonse, zachiphamaso, kaduka ndi mtundu uliwonse wa miseche.+