Miyambo 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nyumba yake ndiyo njira ya ku Manda.+ Imatsikira kuzipinda za imfa.+