Miyambo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mapazi ake amatsikira ku imfa.+ Miyendo yake imalowera ku Manda.+ Miyambo 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma mwamunayo sakudziwa kuti kumeneko kuli akufa, ndiponso kuti amene amaitanidwa ndi mkaziyu ali kumalo otsika a ku Manda.+
18 Koma mwamunayo sakudziwa kuti kumeneko kuli akufa, ndiponso kuti amene amaitanidwa ndi mkaziyu ali kumalo otsika a ku Manda.+