Nyimbo ya Solomo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Khungu lako lilinso ngati kasupe wa m’munda, chitsime cha madzi abwino,+ ndiponso timitsinje tochokera ku Lebanoni.+ 1 Akorinto 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwamuna azipereka kwa mkazi wake mangawa ake,+ mkazinso achite chimodzimodzi kwa mwamuna wake.+ Aheberi 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+
15 Khungu lako lilinso ngati kasupe wa m’munda, chitsime cha madzi abwino,+ ndiponso timitsinje tochokera ku Lebanoni.+
4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+