1 Akorinto 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma chifukwa cha kuwanda kwa dama,*+ mwamuna aliyense akhale ndi mkazi wakewake+ ndipo mkazi aliyense akhale ndi mwamuna wakewake. 1 Akorinto 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musamanane,+ kupatulapo ngati mwagwirizana kuimitsa kaye mangawawo kwa nthawi yodziwika,+ kuti muthere nthawi pa kupemphera, kenako mukhalenso mwa nthawi zonse, kuopera kuti Satana angapitirize kumakuyesani+ mukalephera kudzigwira.+
2 Koma chifukwa cha kuwanda kwa dama,*+ mwamuna aliyense akhale ndi mkazi wakewake+ ndipo mkazi aliyense akhale ndi mwamuna wakewake.
5 Musamanane,+ kupatulapo ngati mwagwirizana kuimitsa kaye mangawawo kwa nthawi yodziwika,+ kuti muthere nthawi pa kupemphera, kenako mukhalenso mwa nthawi zonse, kuopera kuti Satana angapitirize kumakuyesani+ mukalephera kudzigwira.+