1 Akorinto 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma chifukwa cha kufala kwa chiwerewere,* mwamuna aliyense akhale ndi mkazi wakewake+ ndipo mkazi aliyense akhale ndi mwamuna wakewake.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:2 Chinsinsi cha Banja, ptsa. 156-157 Galamukani!,5/8/1991, tsa. 29
2 Koma chifukwa cha kufala kwa chiwerewere,* mwamuna aliyense akhale ndi mkazi wakewake+ ndipo mkazi aliyense akhale ndi mwamuna wakewake.+