Miyambo 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mwana wanga, ukamvera mawu anga+ ndi kusunga malamulo anga ngati chuma chamtengo wapatali,+ Miyambo 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ananu, mverani malangizo* a bambo anu.+ Mvetserani kuti mupeze luso lomvetsa zinthu.+ Miyambo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwana wanga, mvetsera nzeru zanga.+ Tchera makutu ako ku zimene ndikukuphunzitsa zokhudza kuzindikira,+ Luka 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komano zogwera panthaka yabwino, ndi anthu amene pambuyo pomva mawuwo ndi mtima woona+ komanso wabwino, amawagwiritsitsa ndi kubereka zipatso mwa kupirira.+
5 Mwana wanga, mvetsera nzeru zanga.+ Tchera makutu ako ku zimene ndikukuphunzitsa zokhudza kuzindikira,+
15 Komano zogwera panthaka yabwino, ndi anthu amene pambuyo pomva mawuwo ndi mtima woona+ komanso wabwino, amawagwiritsitsa ndi kubereka zipatso mwa kupirira.+