Salimo 119:101 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 101 Ndaletsa mapazi anga kuyenda m’njira iliyonse yoipa.+Ndachita izi kuti ndisunge mawu anu.+ Miyambo 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usakhotere kudzanja lamanja kapena lamanzere.+ Chotsa phazi lako pa zoipa.+ 1 Akorinto 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musasocheretsedwe. Kugwirizana ndi anthu oipa kumawononga makhalidwe abwino.+