Miyambo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Njira yako ikhale kutali ndi iye. Usayandikire pakhomo la nyumba yake,+ 1 Petulo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Okondedwa, popeza ndinu alendo ndiponso anthu osakhalitsa m’dzikoli,+ ndikukudandaulirani kuti muzipewa zilakolako za thupi+ zimene zili pa nkhondo yolimbana ndi moyo.+
11 Okondedwa, popeza ndinu alendo ndiponso anthu osakhalitsa m’dzikoli,+ ndikukudandaulirani kuti muzipewa zilakolako za thupi+ zimene zili pa nkhondo yolimbana ndi moyo.+