Salimo 37:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma anthu ofatsa adzalandira dziko lapansi,+Ndipo adzasangalala ndi mtendere wochuluka.+ Mateyu 25:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Pamenepo mfumu idzauza a kudzanja lake lamanja kuti, ‘Bwerani, inu amene mwadalitsidwa ndi Atate+ wanga. Lowani+ mu ufumu+ umene anakonzera inu kuchokera pa kukhazikitsidwa kwa dziko.+
34 “Pamenepo mfumu idzauza a kudzanja lake lamanja kuti, ‘Bwerani, inu amene mwadalitsidwa ndi Atate+ wanga. Lowani+ mu ufumu+ umene anakonzera inu kuchokera pa kukhazikitsidwa kwa dziko.+