Salimo 94:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zindikirani anthu opanda nzeru inu.+Ndipo opusa inu, mudzakhala liti ozindikira?+ Luka 19:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Iye anati: “Iwe ukanazindikira+ lero zinthu zamtendere . . . koma tsopano zabisika kuti usathe kuziona.+
42 Iye anati: “Iwe ukanazindikira+ lero zinthu zamtendere . . . koma tsopano zabisika kuti usathe kuziona.+