Salimo 50:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Umakhala pansi ndi kunenera m’bale wako zinthu zoipa,+Umapezera zifukwa mwana wamwamuna wa mayi ako.+ Salimo 101:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Aliyense wonenera mnzake miseche,+Ndimamukhalitsa chete.+Sindingathe kupirira zochita za+Aliyense wodzikweza ndi wamtima wonyada.+
20 Umakhala pansi ndi kunenera m’bale wako zinthu zoipa,+Umapezera zifukwa mwana wamwamuna wa mayi ako.+
5 Aliyense wonenera mnzake miseche,+Ndimamukhalitsa chete.+Sindingathe kupirira zochita za+Aliyense wodzikweza ndi wamtima wonyada.+