Miyambo 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+ Miyambo 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Milomo yolungama imasangalatsa mfumu yaikulu,+ ndipo mfumuyo imakonda munthu wolankhula zinthu zowongoka.+ Mateyu 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chake chabwino,+ koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa.+
18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+
13 Milomo yolungama imasangalatsa mfumu yaikulu,+ ndipo mfumuyo imakonda munthu wolankhula zinthu zowongoka.+
35 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chake chabwino,+ koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa.+