Yobu 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi si paja wochita zoipa amakumana ndi zosautsa,+Ndipo ochitira anzawo zopweteka tsoka limawagwera? Salimo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amadziwa njira za olungama,+Koma oipa adzatheratu pamodzi ndi njira zawo.+ Luka 13:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma iye adzakuuzani kuti, ‘Sindikudziwa kumene mukuchokera. Ndichokereni pano, nonsenu ochita zinthu zosalungama!’+ Aroma 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma adzapereka chilango ndi mkwiyo+ kwa okonda mikangano+ amenenso samvera choonadi+ koma amamvera zosalungama.
3 Kodi si paja wochita zoipa amakumana ndi zosautsa,+Ndipo ochitira anzawo zopweteka tsoka limawagwera?
27 Koma iye adzakuuzani kuti, ‘Sindikudziwa kumene mukuchokera. Ndichokereni pano, nonsenu ochita zinthu zosalungama!’+
8 Koma adzapereka chilango ndi mkwiyo+ kwa okonda mikangano+ amenenso samvera choonadi+ koma amamvera zosalungama.