Miyambo 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mawu a m’kamwa mwa munthu ndiwo madzi akuya.+ Chitsime cha nzeru chili ngati mtsinje wosefukira.+ Machitidwe 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndidzatsanuliranso mbali ya mzimu wanga ngakhale pa akapolo anga aamuna ndi aakazi m’masiku amenewo, ndipo iwo adzanenera.+
18 Ndidzatsanuliranso mbali ya mzimu wanga ngakhale pa akapolo anga aamuna ndi aakazi m’masiku amenewo, ndipo iwo adzanenera.+