Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 11:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Koma Mose anayankha kuti: “Kodi ukuchita nsanje chifukwa chondidera nkhawa? Ayi usatero. Ndikanakonda anthu onse a Yehova akanakhala aneneri, chifukwa Yehova akanaika mzimu wake pa iwo!”+

  • Yoweli 2:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Masiku amenewo ndidzatsanuliranso mzimu wanga pa antchito anu aamuna ndi aakazi.+

  • Machitidwe 21:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Titafufuza tinapeza ophunzira ndi kukhala nawo kumeneko masiku 7. Koma mouziridwa ndi mzimu,+ iwo anauza Paulo mobwerezabwereza kuti asakaponde mu Yerusalemu.

  • 1 Akorinto 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Winanso amapatsidwa mphatso yochita ntchito zamphamvu,+ wina kunenera,+ wina kuzindikira+ mawu ouziridwa,+ wina kulankhula malilime osiyanasiyana,+ ndiponso wina kumasulira+ malilime.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena