Salimo 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+Koma kukoma mtima kwake ndi kwa moyo wonse.+Usiku kumakhala kulira,+ koma m’mawa kumakhala kufuula ndi chisangalalo.+ Miyambo 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Wofunafuna kuchitira ena zabwino, amafunafuna kuvomerezedwa ndi Mulungu.*+ Koma wofunafuna kuchita zoipa, zoipazo zidzam’bwerera.+
5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+Koma kukoma mtima kwake ndi kwa moyo wonse.+Usiku kumakhala kulira,+ koma m’mawa kumakhala kufuula ndi chisangalalo.+
27 Wofunafuna kuchitira ena zabwino, amafunafuna kuvomerezedwa ndi Mulungu.*+ Koma wofunafuna kuchita zoipa, zoipazo zidzam’bwerera.+