Salimo 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mtima wanga wosagawanika ndiponso wowongoka unditeteze,+Pakuti chiyembekezo changa chili mwa inu.+ Salimo 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiweruzeni,+ inu Yehova, pakuti ine ndayenda mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika,+Ndipo ndikudalira Yehova kuti ndisagwedezeke.+ Miyambo 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chilungamo chimateteza munthu amene sachita zopweteka ena,+ koma wochimwa amawonongedwa ndi zoipa.+
21 Mtima wanga wosagawanika ndiponso wowongoka unditeteze,+Pakuti chiyembekezo changa chili mwa inu.+
26 Ndiweruzeni,+ inu Yehova, pakuti ine ndayenda mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika,+Ndipo ndikudalira Yehova kuti ndisagwedezeke.+
6 Chilungamo chimateteza munthu amene sachita zopweteka ena,+ koma wochimwa amawonongedwa ndi zoipa.+