-
Yeremiya 40:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Tsopano taona! Lero ndakumasula maunyolo amene anali m’manja mwako. Ngati ungakonde kutsagana nane ku Babulo tiye, ndipo ndidzakuyang’anira.+ Koma ngati sungakonde kutsagana nane ku Babulo, tsala. Taona! Dziko lonse lili pamaso pako. Pita kulikonse kumene ungaone kuti n’kwabwino, kulikonse kumene ungakonde kupita.”+
-