Yeremiya 40:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Lero ndikumasula maunyolo amene ali mʼmanja mwako. Ngati ungakonde kupita nane ku Babulo, tiye ndipo ndizikakuyangʼanira. Koma ngati sukufuna kupita nane ku Babulo, usapite. Taona! Dziko lonse lili pamaso pako. Pita kulikonse kumene ungakonde.”+
4 Lero ndikumasula maunyolo amene ali mʼmanja mwako. Ngati ungakonde kupita nane ku Babulo, tiye ndipo ndizikakuyangʼanira. Koma ngati sukufuna kupita nane ku Babulo, usapite. Taona! Dziko lonse lili pamaso pako. Pita kulikonse kumene ungakonde.”+