Miyambo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwana wanga, ngati walonjeza kuti udzapereka ngongole ya mnzako iye akadzalephera kubweza,+ ngati wagwirana chanza ndi mlendo pochita mgwirizano,+ Miyambo 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amagwirana chanza ndi munthu wina,+ ndipo amalonjeza pamaso pa mnzake kuti iye akhala chikole.+ Miyambo 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ngati munthu walonjeza kuti akhala chikole kwa mlendo,+ umulande chovala chake. Ndiponso wochita zoipa ndi mkazi wachilendo umulande chikole.+ Miyambo 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Usakhale pakati pa anthu ogwirana chanza,+ pakati pa anthu amene amakhala chikole cha ngongole za anthu ena.+
6 Mwana wanga, ngati walonjeza kuti udzapereka ngongole ya mnzako iye akadzalephera kubweza,+ ngati wagwirana chanza ndi mlendo pochita mgwirizano,+
18 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amagwirana chanza ndi munthu wina,+ ndipo amalonjeza pamaso pa mnzake kuti iye akhala chikole.+
16 Ngati munthu walonjeza kuti akhala chikole kwa mlendo,+ umulande chovala chake. Ndiponso wochita zoipa ndi mkazi wachilendo umulande chikole.+
26 Usakhale pakati pa anthu ogwirana chanza,+ pakati pa anthu amene amakhala chikole cha ngongole za anthu ena.+