Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 17:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Chonde, mundisungire chotsimikizira changa.+

      Palinso ndani amene angagwirane nane chanza+ monga chikole?

  • Miyambo 6:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mwana wanga, ngati walonjeza kuti udzapereka ngongole ya mnzako iye akadzalephera kubweza,+ ngati wagwirana chanza ndi mlendo pochita mgwirizano,+

  • Miyambo 11:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Munthu amene walonjeza kuti adzapereka ngongole ya mlendo iye akadzalephera kubweza,+ zinthu sizidzamuyendera bwino. Koma wodana ndi kugwirana chanza pochita mgwirizano sakhala ndi nkhawa.

  • Miyambo 22:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Usakhale pakati pa anthu ogwirana chanza,+ pakati pa anthu amene amakhala chikole cha ngongole za anthu ena.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena