Miyambo 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zoyembekezera za olungama zimasangalatsa,+ koma chiyembekezo cha oipa chidzawonongeka.+ 2 Atesalonika 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango+ cha chiwonongeko chamuyaya,+ kuwachotsa pamaso pa Ambuye ndi ku ulemerero wa mphamvu zake.+ Aheberi 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma pali chiyembekezo china choopsa cha chiweruzo,+ ndiponso pali nsanje yoyaka moto imene idzawononge otsutsawo.+
9 Amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango+ cha chiwonongeko chamuyaya,+ kuwachotsa pamaso pa Ambuye ndi ku ulemerero wa mphamvu zake.+
27 Koma pali chiyembekezo china choopsa cha chiweruzo,+ ndiponso pali nsanje yoyaka moto imene idzawononge otsutsawo.+