Salimo 112:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Woipa adzaona zimenezi ndipo adzasautsika.+ ש [Shin]Adzakukuta mano ndi kusungunuka.+ ת [Taw]Chikhumbo cha anthu oipa chidzatha.+ Miyambo 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu woipa akafa, chiyembekezo chake chimawonongeka,+ ndipo zimene anali kuyembekezera kuchokera ku mphamvu zake sizichitika.+ Mateyu 25:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo iwowa adzachoka kupita ku chiwonongeko chotheratu,+ koma olungama ku moyo wosatha.”+ 2 Atesalonika 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango+ cha chiwonongeko chamuyaya,+ kuwachotsa pamaso pa Ambuye ndi ku ulemerero wa mphamvu zake.+
10 Woipa adzaona zimenezi ndipo adzasautsika.+ ש [Shin]Adzakukuta mano ndi kusungunuka.+ ת [Taw]Chikhumbo cha anthu oipa chidzatha.+
7 Munthu woipa akafa, chiyembekezo chake chimawonongeka,+ ndipo zimene anali kuyembekezera kuchokera ku mphamvu zake sizichitika.+
9 Amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango+ cha chiwonongeko chamuyaya,+ kuwachotsa pamaso pa Ambuye ndi ku ulemerero wa mphamvu zake.+