Miyambo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Waulesi amalakalaka zinthu, chonsecho moyo wake ulibe chilichonse.+ Koma anthu akhama adzanenepa.+ Miyambo 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu waulesi amapisa dzanja lake m’mbale yodyera, koma amalephera kulibweretsa pakamwa pake chifukwa amaona kuti n’zotopetsa kwambiri.+
15 Munthu waulesi amapisa dzanja lake m’mbale yodyera, koma amalephera kulibweretsa pakamwa pake chifukwa amaona kuti n’zotopetsa kwambiri.+