Miyambo 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu waulesi amapisa dzanja lake m’mbale yodyera,+ koma n’kulephera kulibweretsa pakamwa.+