Salimo 69:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndatopa ndi kufuula kwanga,+Mawu asasa pammero panga.Maso anga achita mdima poyembekezera Mulungu wanga.+ Salimo 143:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Fulumirani, ndiyankheni inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.+Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+
3 Ndatopa ndi kufuula kwanga,+Mawu asasa pammero panga.Maso anga achita mdima poyembekezera Mulungu wanga.+
7 Fulumirani, ndiyankheni inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.+Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+