Afilipi 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo ine ndikupitiriza kupemphera kuti chikondi chanu chipitirire kukula,+ limodzi ndi kudziwa zinthu molondola,+ komanso kuzindikira zinthu bwino kwambiri.+ 2 Timoteyo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Uziganizira zimene ndikukuuzazi nthawi zonse. Ndithudi, Ambuye adzakuthandiza kuzindikira+ zinthu zonse.
9 Ndipo ine ndikupitiriza kupemphera kuti chikondi chanu chipitirire kukula,+ limodzi ndi kudziwa zinthu molondola,+ komanso kuzindikira zinthu bwino kwambiri.+
7 Uziganizira zimene ndikukuuzazi nthawi zonse. Ndithudi, Ambuye adzakuthandiza kuzindikira+ zinthu zonse.