Miyambo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munthu amene wapeza mtima wanzeru+ akukonda moyo wake. Wopitiriza kusonyeza kuzindikira amapeza zabwino.+ Mateyu 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Chotero aliyense wakumva mawu angawa ndi kuwachita adzafanizidwa ndi munthu wochenjera, amene anamanga nyumba yake pathanthwe.+ Aheberi 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti bambo athu otiberekawo, kwa masiku ochepa anali kutilanga malinga ndi zimene anaziona kuti n’zoyenera,+ koma Mulungu amatilanga kuti tipindule ndiponso kuti tikhale oyera ngati iyeyo.+
8 Munthu amene wapeza mtima wanzeru+ akukonda moyo wake. Wopitiriza kusonyeza kuzindikira amapeza zabwino.+
24 “Chotero aliyense wakumva mawu angawa ndi kuwachita adzafanizidwa ndi munthu wochenjera, amene anamanga nyumba yake pathanthwe.+
10 Pakuti bambo athu otiberekawo, kwa masiku ochepa anali kutilanga malinga ndi zimene anaziona kuti n’zoyenera,+ koma Mulungu amatilanga kuti tipindule ndiponso kuti tikhale oyera ngati iyeyo.+