Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 28:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndiyeno anauza munthu kuti,

      ‘Tamvera, kuopa Yehova ndiko nzeru,+

      Ndipo kupatuka pa choipa ndiko kumvetsa zinthu.’”+

  • Miyambo 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+

  • Yeremiya 32:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Ndidzachita nawo pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale+ lakuti sindidzasiya kuwachitira zabwino+ ndipo ndidzawapatsa mtima woti azindiopa kuti asachoke kwa ine.+

  • Chivumbulutso 14:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iye anali kunena mofuula kuti: “Opani Mulungu+ ndi kumupatsa ulemerero,+ chifukwa ola lakuti apereke chiweruzo lafika.+ Chotero lambirani Iye amene anapanga+ kumwamba, dziko lapansi, nyanja, ndi akasupe amadzi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena