Miyambo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Woyenda ndi mtima wosagawanika adzayenda popanda chomuopseza,+ koma wokhotetsa njira zake adzadziwika.+ Machitidwe 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Iye amalandira munthu wochokera mu mtundu uliwonse, amene amamuopa ndi kuchita chilungamo.+ Aheberi 10:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Tsopano, ife si mtundu wa anthu obwerera m’mbuyo kupita kuchiwonongeko,+ koma mtundu wa anthu okhala ndi chikhulupiriro chosunga moyo.+
9 Woyenda ndi mtima wosagawanika adzayenda popanda chomuopseza,+ koma wokhotetsa njira zake adzadziwika.+
39 Tsopano, ife si mtundu wa anthu obwerera m’mbuyo kupita kuchiwonongeko,+ koma mtundu wa anthu okhala ndi chikhulupiriro chosunga moyo.+