Miyambo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chigamulo chochokera kwa Mulungu chizikhala palilime la mfumu poweruza milandu.+ Pakamwa pake pazikhala pokhulupirika.+ Miyambo 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mtsogoleri akamamvera mabodza, onse omutumikira adzakhala oipa.+
10 Chigamulo chochokera kwa Mulungu chizikhala palilime la mfumu poweruza milandu.+ Pakamwa pake pazikhala pokhulupirika.+