Deuteronomo 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Akakhala pampando wachifumu, ayenera kukopera buku lakelake la chilamulo ichi, kuchokera m’buku limene ansembe achilevi amasunga.+ 2 Samueli 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mzimu wa Yehova unandilankhulitsa,+Ndipo mawu ake anali palilime langa.+ 1 Mafumu 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Aisiraeli onse anamva za chigamulo+ chimene mfumu inapereka, ndipo anachita mantha chifukwa cha mfumuyo,+ popeza anaona kuti nzeru+ za Mulungu zinali mwa iye kuti azipereka zigamulo. Salimo 72:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Inu Mulungu, dziwitsani mfumu za zigamulo zanu,+Ndipo dziwitsani mwana wa mfumu za chilungamo chanu.+
18 Akakhala pampando wachifumu, ayenera kukopera buku lakelake la chilamulo ichi, kuchokera m’buku limene ansembe achilevi amasunga.+
28 Aisiraeli onse anamva za chigamulo+ chimene mfumu inapereka, ndipo anachita mantha chifukwa cha mfumuyo,+ popeza anaona kuti nzeru+ za Mulungu zinali mwa iye kuti azipereka zigamulo.
72 Inu Mulungu, dziwitsani mfumu za zigamulo zanu,+Ndipo dziwitsani mwana wa mfumu za chilungamo chanu.+