Miyambo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuopa Yehova ndiko chiyambi cha kudziwa zinthu.+ Nzeru ndi malangizo zimanyozedwa ndi zitsiru.*+ Miyambo 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 chifukwa chakuti anadana ndi kudziwa zinthu+ ndipo sanasankhe kuopa Yehova.+ Miyambo 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mtsogoleri amene ali wosazindikira kwenikweni amakhalanso wakatangale kwambiri,+ koma munthu wodana ndi phindu lachinyengo+ adzachulukitsa masiku ake.
16 Mtsogoleri amene ali wosazindikira kwenikweni amakhalanso wakatangale kwambiri,+ koma munthu wodana ndi phindu lachinyengo+ adzachulukitsa masiku ake.