Miyambo 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wogwira ntchito ndi dzanja laulesi adzakhala wosauka,+ koma dzanja la munthu wakhama ndi limene limalemeretsa.+ Aroma 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musakhale aulesi pa ntchito yanu.+ Yakani ndi mzimu.+ Tumikirani Yehova monga akapolo.+
4 Wogwira ntchito ndi dzanja laulesi adzakhala wosauka,+ koma dzanja la munthu wakhama ndi limene limalemeretsa.+