Deuteronomo 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 muzifunafuna, kufufuza ndi kufunsitsa za nkhani imeneyo.+ Mukapeza kuti ndi zoonadi, choipa chimenechi chachitikadi pakati panu, 2 Samueli 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Poyankha anati: “Mbuyanga mfumu, mtumiki wanga ndi amene anandipusitsa. Ine mtumiki wanu+ ndinanena kuti, ‘Ndiikireni chishalo pabulu wamkazi kuti ndikwerepo ndi kupita pamodzi ndi mfumu,’ pakuti ine mtumiki wanu ndine wolumala.+ Miyambo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usamapite kukazenga mlandu mofulumira, pakuti udzachita chiyani pamapeto pake mnzakoyo akakuchititsa manyazi?+
14 muzifunafuna, kufufuza ndi kufunsitsa za nkhani imeneyo.+ Mukapeza kuti ndi zoonadi, choipa chimenechi chachitikadi pakati panu,
26 Poyankha anati: “Mbuyanga mfumu, mtumiki wanga ndi amene anandipusitsa. Ine mtumiki wanu+ ndinanena kuti, ‘Ndiikireni chishalo pabulu wamkazi kuti ndikwerepo ndi kupita pamodzi ndi mfumu,’ pakuti ine mtumiki wanu ndine wolumala.+
8 Usamapite kukazenga mlandu mofulumira, pakuti udzachita chiyani pamapeto pake mnzakoyo akakuchititsa manyazi?+