Mlaliki 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi munthu amapeza phindu lanji pa ntchito yake yonse yovuta, imene amaigwira+ mwakhama padziko lapansi pano?*+ Mlaliki 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Palinso chinthu china chomvetsa chisoni kwambiri: Monga mmene munthu anabwerera, adzapitanso chimodzimodzi. Kodi pali phindu lanji kwa munthu amene amachita khama kugwirira ntchito mphepo?+
3 Kodi munthu amapeza phindu lanji pa ntchito yake yonse yovuta, imene amaigwira+ mwakhama padziko lapansi pano?*+
16 Palinso chinthu china chomvetsa chisoni kwambiri: Monga mmene munthu anabwerera, adzapitanso chimodzimodzi. Kodi pali phindu lanji kwa munthu amene amachita khama kugwirira ntchito mphepo?+