Salimo 119:90 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 90 Kukhulupirika kwanu kudzakhalapobe ku mibadwomibadwo.+Mwakhazikitsa mwamphamvu dziko lapansi, kuti lisagwedezeke.+ Aefeso 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Izi n’zogwirizana ndi cholinga chamuyaya chimene iye anakhala nacho chokhudza Khristuyo,+ yemwe ndi Yesu Ambuye wathu.
90 Kukhulupirika kwanu kudzakhalapobe ku mibadwomibadwo.+Mwakhazikitsa mwamphamvu dziko lapansi, kuti lisagwedezeke.+
11 Izi n’zogwirizana ndi cholinga chamuyaya chimene iye anakhala nacho chokhudza Khristuyo,+ yemwe ndi Yesu Ambuye wathu.