Salimo 141:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nditetezeni kuti ndisagwidwe pamsampha umene anditchera,+Kuti ndisakodwe ndi makhwekhwe a anthu ochita zopweteka anzawo.+ Salimo 142:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mvetserani kulira kwanga kochonderera,+Pakuti ndasautsika koopsa.+Ndipulumutseni kwa anthu amene akundizunza,+Pakuti iwo ndi amphamvu kuposa ine.+ Aroma 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tikudziwa tsopano kuti Mulungu amagwirizanitsa zochita zake zonse+ pofuna kupindulitsa amene amakonda Mulungu, anthu oitanidwa mogwirizana ndi cholinga chake.+
9 Nditetezeni kuti ndisagwidwe pamsampha umene anditchera,+Kuti ndisakodwe ndi makhwekhwe a anthu ochita zopweteka anzawo.+
6 Mvetserani kulira kwanga kochonderera,+Pakuti ndasautsika koopsa.+Ndipulumutseni kwa anthu amene akundizunza,+Pakuti iwo ndi amphamvu kuposa ine.+
28 Tikudziwa tsopano kuti Mulungu amagwirizanitsa zochita zake zonse+ pofuna kupindulitsa amene amakonda Mulungu, anthu oitanidwa mogwirizana ndi cholinga chake.+