-
Machitidwe 27:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Titalowanso panyanja kuchokera kumeneko, tinayenda m’mphepete mwa chilumba cha Kupuro chimene chinatitchinjiriza ku mphepo imene inali kuwomba kuchokera kumene ife tinali kupita.
-