-
Yobu 36:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Pakuti iye amakoka madontho a madzi.+
Madonthowo amasefeka n’kutsika ngati mvula ndi nkhungu,
-
Amosi 5:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Yehova ndilo dzina+ la amene anapanga gulu la nyenyezi la Kima+ ndi gulu la nyenyezi la Kesili,+ amene amachititsa mdima wandiweyani+ kukhala kuwala kwa m’mamawa, amenenso amachititsa masana kukhala mdima ngati wausiku,+ amene amaitana madzi akunyanja kuti awakhuthulire panthaka ya dziko lapansi.+
-
-
-